Lyrks
Lyrks
Cover Art

Mtima Lyrics by Achina Gattah Ase

2021

[Chorus: Piksy]
Ndikangokuwona iwe
Mtima wanga kugu-gunda
Nkati ndikusiye pena
Mtima wanga kukufuna
Nde ukangosekelera
Stress umayifufuta
Ukangoti umandikonda
Mtima wanga kutukula

[Verse 1: Achina Gattah Ase]
Natuluka mu shop nsanagule
Namufusa dzina sanatchule
Ndiwe kamwana
Maybe
Nkona ndufuna ndikhale wako baby
Watichani?
Be my queen
Zachamba eti
Kodi mwabwela pa Bimmer yi queen?
Eya
Nanga bwanji ufuna kundikweza njinga?
Monse wayambila kunditchinga
Koma number ndipatseko
Ngati Aircon iwe ndi machine a mphepo
Nane chikondi ndiyeseko
Tiye kunyanja tikapitidwe mphepo
Umu ndi mene ndinapezela love yanga
Five years sakutayitsa nthawi yanga
I don't think it will end in tears
Timayambana koma--

[Chorus: Piksy]
Ndikangokuwona iwe
Mtima wanga kugu-gunda
Nkati ndikusiye pena
Mtima wanga kukufuna
Nde ukangosekelera
Stress umayifufuta
Ukangoti umandikonda
Mtima wanga kutukula

[Verse 2: Gwamba]
Ukangoti "hey" ntima wanga
Usain Bolt
Ndekuti tsiku langa basi walipanga sort
Ukangoti "Bae" olo vep ndimapanga boycott
Koma makape akuyesetsa kuti apeze fault
Koma nkazi wangwiro, mm
Sudziwa Bwandiro, mm
Look ndi nyatwa koma matama ndi zero, mm
With you in my life moyo kufewa ngati pillow
Koma fans imathoka poti Gwambizzle ndi hero
Nde tadekha kaye imva izi dona
Iwe ndi ine ndi limodzi mpaka imvi dona
Ndakhala ndikusakasaka wa CV dona
Pano ndakupeza nde tiye kwa ntiz dona

[Chorus: Piksy]
Ndikangokuwona iwe
Mtima wanga kugu-gunda
Nkati ndikusiye pena
Mtima wanga kukufuna
Nde ukangosekelera
Stress umayifufuta
Ukangoti umandikonda
Mtima wanga kutukula
Ndikagokuwona iwe
Mtima wanga kugu-gunda
Nkati ndikusiye pena
Mtima wanga kukufuna
Nde ukangosekelera
Stress umayifufuta
Ukangoti umandikonda
Mtima wanga kutukula

About “Mtima” by Achina Gattah Ase

Read the complete lyrics to "Mtima" by Achina Gattah Ase in 2021. On Lyrks you can follow along with the full text, explore the artist's discography, and discover related songs. The track is often categorized under Rap.

"Mtima" is performed by Achina Gattah Ase. in 2021 This page provides the full lyric text for fans who want to sing along, study the songwriting, or compare versions across releases. Lyrks organizes lyrics by artist and song slug so you can bookmark and share a stable URL. Music lyrics help listeners connect with emotion, narrative, and rhythm in a track. Whether you are learning English, researching a favorite chorus, or preparing for karaoke, having accurate line breaks and section labels (verse, chorus, bridge) makes the experience easier. We link to the official artist profile on Lyrks where available, including biography snippets, top songs, and chart placements when we have that data. If you enjoy "Mtima", explore more songs by Achina Gattah Ase using the links below. Chart and trending pages on Lyrks highlight what listeners are searching for this week. For copyright or correction requests, see our DMCA and contact pages.

View all songs and biography for Achina Gattah Ase · Trending lyrics · Billboard Hot 100

Frequently asked questions

"Mtima" is credited to Achina Gattah Ase. Songwriting credits may include additional writers listed on the release; check the credits section on this page for linked collaborators.

Album information for "Mtima" is not available in our database yet. You can still read the full lyrics on this page.

Visit the Achina Gattah Ase artist page at /artist/gwamba for biography, popular tracks, and links to more lyric pages.


Lyrks
Lyrks

Your gateway to the world of music lyrics.

Product

Features


© 2026 Lyrks. All rights reserved.