Lyrks
Lyrks
Lyrks
Cover Art

Tuno Lyrics by King Tuzi, Crispy Malawi

2024

[Intro: King Tuzi]
"Amwene"
"Amwene ineyo ndikangomulingalira Tuno amwene"
"Ehe ukamulingalira Tuno chimachitika ndi chani
Abdul with the Sauce
"Ndikangoti ndimuganizire Tuno amwene"
"Ukangoti umuganizire Tuno chimachitika chani?"
"Iwe tayankha eh"
"Tasiya kubanda Tayankha"
"Amwene golide amwene golide eh Tuno amwene"
"Golide wotani?"
"Ndikangoti ndimuganizire Tuno amwene" (Ayy)
"Ndikati golide yokhayo" (Ayy)
(Ayy)
[Chorus :King Tuzi]
Ndapota Ka spliff kukayatsa (eish)
Kundilowa mphuno (utsi) (amwene)
Ndaona chimkazi (mmh hm) ali welo (mmh hm)
Ndikufunika chi cross ngati Bruno (ndipatsile chi cross) (Ayy ay)
Ndilipa magobo daily
Osamabwelela mbuyo (Osamabwelela mbuyo)
They were sleeping on me now amwayi adzuka
Koma ena akadali mtulo
I got a confession I'm crushing on Tuno (eish) (Eh) (Eh) Tuno!(eh)
Tuno! (koma Tuno Ase) (amwene)(mmh)
Tuno!
(Koma Tuno Ase) Ndati Ndaona chi mkazi ali welo
Kufunika chi cross ngati Bruno (eh amwene)
Chi chick cha bho ngati afuna banja (eish) (eish)
Muwuze Andipeze Kuno (tiye nazo)
(Ayy)
(Ayy)
[Verse 1 : King Tuzi]
Tuno
Amwene (amwene) ntagwira uyuyu ndingapenge (ndingapenge) (eish)
Ma member ati ndumayabwa
Akangomva da king ngati aponda chitedze (ngati ndaponda chi cha?)
Tuzi Ku flopper man sizingatheke
Ndayenda ndi Ganja ndukakwera ndege
Zosatheka
Ndimapusha zitheke
She[?] didn't want to feature these rappers keep begging (Let's go)
Ndine mfana wofewa (ofewa) Nsima ndimamwera Fanta (Fanta)
Koma sumandisala spaghetti (sumandisala)
Ndine mfana wozunguza bongo Rasta
Sindiwopa kuvaya ku ndende (sindiwopa kuvaya)
Koma ndendende
Sakumvetsetsa I'm stoned
Ati ah ukufuna umgende? (Ah)
Zandi Wenger ngati coach wa Arsenal
Muyimbire Spe afika anditenge (muyimbire Spe)
Ndati Tuno alikuti? (Alikuti)
In the trap see the way I be rapping
They say I'm the goat ati Tuzi ndi mbuzi (sikunyoza ayi)
Lil shorty bad and she boujee
Let her meet the fam
Kudzamutenga kumudzi
And I just hit another but no dey ain't no strings attached
Palibepo ulusi (palibepo Ka cha?)
Ndili pa TV pa news (uti bwa?)
I'm the goat when it comes to the music
[Chorus : King Tuzi]
Ndapota Ka spliff kukayatsa (eish)
Kundilowa mphuno (utsi) (amwene)
Ndaona chimkazi (mmh hm) ali welo (mmh hm)
Ndikufunika chi cross ngati Bruno (ndipatsile chi cross) (Ayy ay)
Ndilipa magobo daily
Osamabwelela mbuyo (Osamabwelela mbuyo)
They were sleeping on me now amwayi adzuka
Koma ena akadali mtulo
I got a confession I'm crushing on Tuno (eish) (Eh) (Eh) Tuno!(eh)
Tuno! (koma Tuno Ase) (amwene)(mmh)
Tuno!
(Koma Tuno Ase) Ndati Ndaona chi mkazi ali welo
Kufunika chi cross ngati Bruno (eh amwene)
Chi chick cha bho ngati afuna banja (eish)
Muwuze Andipeze Kuno (eish)
(Ayy)
(Ayy)
[Verse 2 : Crispy Malawi]
(Malawian)
Uli ndi Thako kapena umangotha kugwedeza chiuno (hmm?)
Kuyika dollar pa table kuti ndikutengere Ku bedi ngati tulo
Koma sindikuthoka iweyo Tuno
Ndikufuna nzako wachi mbuyo (wachi mbuyo)
Ati Spe ma babe umangosintha ngati kicks
Kodi umamenya Judo?
Hmm
Keep it going keep it moving (vroom vroom)
Ngati sizikuyenda yatsa ma hazard
Zathu zikuyenda tika dropper anthu amangoti ah za Hard (waona)
Zili fly ngati nthakati[?]
Ku north,kumwera ndi pakati (yeah)
Been a player kwa zaka zaka
Pano level yangayi ndi ya Lampard
Ma drinks titha Ku shoppa
Ma Mogo amandipweteka mphuno (mmh) (Tuno)
Utha kushala panja
Ukapota spliff ndi kuzayatsila muno (Tuno)
Koma Na lero olo Nepman sanakambaso za Dzulo?(No Way)
Ife nde tili mkati
Uli panja udya bench ngati ukunyamula zitsulo
(Yeah)
[Chorus :King Tuzi]
Ndapota Ka spliff kukayatsa (eish)
Kundilowa mphuno (utsi) (amwene)
Ndaona chimkazi (mmh hm) ali welo (mmh hm)
Ndikufunika chi cross ngati Bruno (ndipatsile chi cross) (Ayy ay)
Ndilipa magobo daily
Osamabwelela mbuyo (Osamabwelela mbuyo)
They were sleeping on me now amwayi adzuka
Koma ena akadali mtulo
I got a confession I'm crushing on Tuno (eish) (Eh) (Eh) Tuno!(eh)
Tuno! (koma Tuno Ase) (amwene)(mmh)
Tuno!
(Koma Tuno Ase) Ndati Ndaona chi mkazi ali welo
Kufunika chi cross ngati Bruno (eh amwene)
Chi chick cha bho ngati afuna banja (eish)
Muwuze Andipeze Kuno (eish)
(Ayy)
(Ayy)

About “Tuno” by King Tuzi

Read the complete lyrics to "Tuno" by King Tuzi, Crispy Malawi in 2024. On Lyrks you can follow along with the full text, explore the artist's discography, and discover related songs. The track is often categorized under Rap, Malawi, Hip-Hop.

"Tuno" is performed by King Tuzi, Crispy Malawi. in 2024 This page provides the full lyric text for fans who want to sing along, study the songwriting, or compare versions across releases. Lyrks organizes lyrics by artist and song slug so you can bookmark and share a stable URL. Music lyrics help listeners connect with emotion, narrative, and rhythm in a track. Whether you are learning English, researching a favorite chorus, or preparing for karaoke, having accurate line breaks and section labels (verse, chorus, bridge) makes the experience easier. We link to the official artist profile on Lyrks where available, including biography snippets, top songs, and chart placements when we have that data. If you enjoy "Tuno", explore more songs by King Tuzi, Crispy Malawi using the links below. Chart and trending pages on Lyrks highlight what listeners are searching for this week. For copyright or correction requests, see our DMCA and contact pages.

View all songs and biography for King Tuzi · Trending lyrics · Billboard Hot 100

Frequently asked questions

"Tuno" is credited to King Tuzi, Crispy Malawi. Songwriting credits may include additional writers listed on the release; check the credits section on this page for linked collaborators.

Album information for "Tuno" is not available in our database yet. You can still read the full lyrics on this page.

Visit the King Tuzi, Crispy Malawi artist page at /artist/king-tuzi for biography, popular tracks, and links to more lyric pages.