Lyrks
Lyrks
Sign In
Cover Art

Ineyo Lyrics by KwemoGoon

New Wave No Cap (EP)

2020

[Intro]
[?]

[Chorus: KwemoGoon & KingDolla]
Kakuti kathozipha chifukwa cha ineyo
Geliso kusiya chifukwa cha ineyo
Kathawaso kwawo chifukwa cha ineyo
Kati kathobwera ku show chifukwa cha ineyo
Kakuti kathozipha chifukwa cha ineyo
Geliso kusiya chifukwa cha ineyo
Yeah-ah, kathawaso kwawo chifukwa cha ineyo
Kabwera ku show chifukwa cha ineyo, yah

[Verse 1: KwemoGoon & _KingDolla_]
Kakuma talker zosezo, eh
Panopa nde tapanga settle, eh
Kulimba ntima ngati metal, eh
Kufilitsana ngati tomato
Kati kagoma nane ndikhale wake boo
Ndikafuna ku trapper ndizikatenga ku stu'
Tizapange tiana ka Jessy ndi ka Ju'
Nde kamavunga emoji kundiyika mu mood

[Chorus: KwemoGoon & KingDolla]
Kakuti kathozipha chifukwa cha ineyo
Geliso kusiya chifukwa cha ineyo
Kathawaso kwawo chifukwa cha ineyo
Kati kathobwera ku show chifukwa cha ineyo
Kakuti kathozipha chifukwa cha ineyo
Geliso kusiya chifukwa cha ineyo
Yeah-ah, kathawaso kwawo chifukwa cha ineyo
Kabwеra ku show chifukwa cha ineyo, yah

[Verse 2: KwemoGoon & KingDolla]
She say she down for mе kathopanga chilichose (Chili', chili')
Olo 'usiya geli bola ifeyo tikhale tose (Eh, eh, eh, eh)
Kamafila Kwemo no lie (No lie)
Kamandiwuza ngamo each and everyday no lie
Kakuti sikangandisiye
Kangofuna kukhala ndine
Ndikamunda kafuna ndikalime
Kabweleratu kati kazishala ndine
Yah, yah, kangofila star

[Chorus: KwemoGoon & KingDolla]
Kakuti kathozipha chifukwa cha ineyo
Geliso kusiya chifukwa cha ineyo
Kathawaso kwawo chifukwa cha ineyo
Kati kathobwera ku show chifukwa cha ineyo
Kakuti kathozipha chifukwa cha ineyo
Geliso kusiya chifukwa cha ineyo
Yeah-ah, kathawaso kwawo chifukwa cha ineyo
Kabwera ku show chifukwa cha ineyo, yah

[Outro: KwemoGoon]
Chifukwa cha ineyo
Chifukwa cha ineyo
Chifukwa cha ineyo
Credits

About “Ineyo” by KwemoGoon

Read the complete lyrics to "Ineyo" by KwemoGoon from the album "New Wave No Cap (EP)" in 2020. On Lyrks you can follow along with the full text, explore the artist's discography, and discover related songs. The track is often categorized under Rap.

"Ineyo" is performed by KwemoGoon. from the album "New Wave No Cap (EP)" in 2020 This page provides the full lyric text for fans who want to sing along, study the songwriting, or compare versions across releases. Lyrks organizes lyrics by artist and song slug so you can bookmark and share a stable URL. Music lyrics help listeners connect with emotion, narrative, and rhythm in a track. Whether you are learning English, researching a favorite chorus, or preparing for karaoke, having accurate line breaks and section labels (verse, chorus, bridge) makes the experience easier. We link to the official artist profile on Lyrks where available, including biography snippets, top songs, and chart placements when we have that data. If you enjoy "Ineyo", explore more songs by KwemoGoon using the links below. Chart and trending pages on Lyrks highlight what listeners are searching for this week. For copyright or correction requests, see our DMCA and contact pages.

View all songs and biography for KwemoGoon · Trending lyrics · Billboard Hot 100

Frequently asked questions

"Ineyo" is credited to KwemoGoon. Songwriting credits may include additional writers listed on the release; check the credits section on this page for linked collaborators.

"Ineyo" appears on "New Wave No Cap (EP)" in 2020.

Visit the KwemoGoon artist page at /artist/kwemogoon for biography, popular tracks, and links to more lyric pages.


Lyrks
Lyrks

Your gateway to the world of music lyrics.

Product

Features


© 2026 Lyrks. All rights reserved.