Lyrks
Lyrks
Lyrks
Cover Art

Chelele Lyrics by Molto zambia

Chelele

2020

VERSE 1
Ndinapti n'kasakile ma ganyu /
Ku Lusaka amai tionane/
Ndi guleko ma bikiloni a new/
Kumudzi ugh! Kulije money/
Talema kudyela munkhwani, Chambo, Kachumbari ndi bonongwe /
Mundi sungile bwino bulu langa, nondi pemphelela kukacha ngwee /
A Mesiya az'ingo dutsa nane, kwa ine pomwe ndi saka money /
For his blessings to shower me mu nthawi ya mvula ndi sanane /
Lekani kulila amai Chete, conde musa sakamane /
Am about to make the family proud ndikhulupirira musadande /
Ndi londole, ndi bodole, za banja langa n'kuti /
Ndi bwela ndi galimoto agogo zolima n'kulonga mubuti /
Apo ndishi ndine mponda matiki taleka n'fuula njuchi /
Nati ni ponye sitepe ni chinje zinthu pakuti /
CHORUS
Amama alulila mabvuto achuluka aza cita bwanji ehh /
Linagoma chimbira, tsono thonje akuti azalima bwanji ehh /
Tsiku ndi caka, mwеzi ndi zaka ng'ombe nazo zingo buula ehh /
Nda langa kumwamba conde malipiliro apa mwеzi ndi machenji ehh /
Ooooh conde amama musalile /
Ooooh conde Adada zaine /
Ooooh conde Agogo musalile /
Ooooh conde Abanja zaine /
VERSE 2
Yeo Amama Kodi Kumudzi bwanji uko /
Boma inawa ninkha Atata fataleza uko /
Chabwino kumva koma nane ndili bho /
Pepa ninali chete, zii sini napange call /
Papita mwezi khumi lomba, ndi kungo joba, ena aona ndi zoba /
Pa Lusaka umoyo lomba, kucita soka, abanja ndikali lova /
Ayi conde sizipopa, mutu wokoka, ndilu kankha ngati Rover /
Yehovah ndikalu konkha, Kopanda ku oonjoka, tsiku lina aza sova /
Mphaka tonse mbanja lathu tika bvale nsuti /
Nthawi zonse ndima uza Amai N'kuti /
BRIDGE
Tsiku lina ndi zadya ndi Mfumu /
Pa mbale imodzi sauce chi phumu /
Kunena Yesu ndinu M'kulu /
Ku dutsa mo jeda-jeda conde ndikuti /
CHORUS
Amama alulila mabvuto achuluka aza cita bwanji ehh /
Linagoma chimbira, tsono thonje akuti azalima bwanji ehh /
Tsiku ndi caka, mwezi ndi zaka ng'ombe nazo zingo buula ehh /
Nda langa kumwamba conde malipiliro apa mwezi ndi machenji ehh /
Ooooh conde amama musalile /
Ooooh conde Adada zaine /
Ooooh conde Agogo musalile /
Ooooh conde Abanja zaine /

About “Chelele” by Molto zambia

Read the complete lyrics to "Chelele" by Molto zambia from the album "Chelele" in 2020. On Lyrks you can follow along with the full text, explore the artist's discography, and discover related songs. The track is often categorized under Rap.

"Chelele" is performed by Molto zambia. from the album "Chelele" in 2020 This page provides the full lyric text for fans who want to sing along, study the songwriting, or compare versions across releases. Lyrks organizes lyrics by artist and song slug so you can bookmark and share a stable URL. Music lyrics help listeners connect with emotion, narrative, and rhythm in a track. Whether you are learning English, researching a favorite chorus, or preparing for karaoke, having accurate line breaks and section labels (verse, chorus, bridge) makes the experience easier. We link to the official artist profile on Lyrks where available, including biography snippets, top songs, and chart placements when we have that data. If you enjoy "Chelele", explore more songs by Molto zambia using the links below. Chart and trending pages on Lyrks highlight what listeners are searching for this week. For copyright or correction requests, see our DMCA and contact pages.

View all songs and biography for Molto zambia · Trending lyrics · Billboard Hot 100

Frequently asked questions

"Chelele" is credited to Molto zambia. Songwriting credits may include additional writers listed on the release; check the credits section on this page for linked collaborators.

"Chelele" appears on "Chelele" in 2020.

Visit the Molto zambia artist page at /artist/molto-zambia for biography, popular tracks, and links to more lyric pages.