Lyrks
Lyrks
Cover Art

Dzuwa Lisanalowe Lyrics by Suckle

2018

INTRO(Hazel & Suckle)

Yey yeh yeh yeeeh!
Hehe..! Suckle, is all oh well!
Kanyamata kanyamwale
Its your boy Hazel

VERSE 1(Suckle)

Aaa! Life yanga ndichi testimony//
Kukhala ndi moyo ndichisomo choti//
Wangondikondera ndine wake mmodzi//
Onyozetsa dzina lake you can guess it homie//
Koma kumwamba tikafika//
Moyo wamazuzo ku Africa//
Ongodzadza ndi imfa ndi matenda bruh//
Dzuwa Lisanalowe Yesu ndiye yankho man//
Mtsogoleri wa ochimwa//
Watsogolo lowala koma pano linathima//
Nkhani ndikolowera ulendowu ndiwosayima//
Okomedwa atsalira ulendowu ndiwamtima//
Ima!Usavere dziko samala ndipo//
Dikira usakhale ndipo dolo wa tchimo//
Imfa yake yapantanda ndika daily good news//
Pano pride yatipha all the BA's are fools//

HOOK(Hazel)

Lisanalowe dzuwa Atate ndikufuna(mukhale nane!)
Chisomo chanu Atate eeeh! (Chifike pa ine!)
Lisanalowe dzuwa Atate ndikufuna (mukhale nane!)
Chisomo chanu Atate ooh! Ooo ooh!  
.
Dzuwa Lisanalowe eeeeh!(Zambiri zimachitika yeh yeh!Nkhondo kaduka nsanje iyee!)/
Pena ndimadera nkhawaaa(Ndimalingalira ndapanga chani chomusangalatsa Yahwe dzuwa lisanalowe)/

VERSE 2(Suckle)

Eya Lisanalowe pavuta ndi pati//
Ndine sin master ndikusaka mwazi//
Wake wapantanda unditsuke basi//
Hell fire simatengera ali ndi dazi//
Wayamba ntchito mwa ife sangasiyire pompo//
Olo ntakhala wa up town opanda inu local//
Inuyo ndima key awamumtima wanga lock//
Mukatseka mu mtima zachikunja zonse nono//
Oh God! Dzuwa Lisanalowe ndimasowa mphamvu//
Yochita zofuna zanu moyo uli wefuu//
This life Is full of mercies life full of grace//
Ochimwa olungama onse mtendere amawupeza//
Dzuwa Lisanalowe life yanga nde ndi bomba(bomb)//
Simachedwa kuphulika ka mistake ka pompa//
Dzuwa Lisanalowe life yanga nde ndi bomba(bomb) //
Simachedwa kuphulika ka mistake ka pompa//

HOOK(Hazel)

Lisanalowe dzuwa Atate ndikufuna(mukhale nane!)
Chisomo chanu Atate eeeh! (Chifike pa ine!)
Lisanalowe dzuwa Atate ndikufuna (mukhale nane!)
Chisomo chanu Atate ooh! Ooo ooh!  
.
Dzuwa Lisanalowe eeeeh!(Zambiri zimachitika yeh yeh!Nkhondo kaduka nsanje iyee!)/
Pena ndimadera nkhawaaa(Ndimalingalira ndapanga chani chomusangalatsa Yahwe dzuwa lisanalowe)/

VERSE 3(Hazel)

Our father who art in heaven//
Hallowed be thy name//
Dzuwa Lisanalowe mukhale nafe//
Chotsani kaduka ndi nsanje//
Mutipatse zosowa zathu//
Bring unity among us God//
Dzuwa lisanalowe mukhale nafe eee! Dzuwa!! //

HOOK(Hazel)

Lisanalowe dzuwa Atate ndikufuna(mukhale nane!)
Chisomo chanu Atate eeeh! (Chifike pa ine!)
Lisanalowe dzuwa Atate ndikufuna (mukhale nane!)
Chisomo chanu Atate ooh! Ooo ooh!  
.
Dzuwa Lisanalowe eeeeh!(Zambiri zimachitika yeh yeh!Nkhondo kaduka nsanje iyee!)/
Pena ndimadera nkhawaaa(Ndimalingalira ndapanga chani chomusangalatsa Yahwe dzuwa lisanalowe!)
Credits

About “Dzuwa Lisanalowe” by Suckle

Read the complete lyrics to "Dzuwa Lisanalowe" by Suckle in 2018. On Lyrks you can follow along with the full text, explore the artist's discography, and discover related songs. The track is often categorized under Rap.

"Dzuwa Lisanalowe" is performed by Suckle. in 2018 This page provides the full lyric text for fans who want to sing along, study the songwriting, or compare versions across releases. Lyrks organizes lyrics by artist and song slug so you can bookmark and share a stable URL. Music lyrics help listeners connect with emotion, narrative, and rhythm in a track. Whether you are learning English, researching a favorite chorus, or preparing for karaoke, having accurate line breaks and section labels (verse, chorus, bridge) makes the experience easier. We link to the official artist profile on Lyrks where available, including biography snippets, top songs, and chart placements when we have that data. If you enjoy "Dzuwa Lisanalowe", explore more songs by Suckle using the links below. Chart and trending pages on Lyrks highlight what listeners are searching for this week. For copyright or correction requests, see our DMCA and contact pages.

View all songs and biography for Suckle · Trending lyrics · Billboard Hot 100

Frequently asked questions

"Dzuwa Lisanalowe" is credited to Suckle. Songwriting credits may include additional writers listed on the release; check the credits section on this page for linked collaborators.

Album information for "Dzuwa Lisanalowe" is not available in our database yet. You can still read the full lyrics on this page.

Visit the Suckle artist page at /artist/suckle for biography, popular tracks, and links to more lyric pages.


Lyrks
Lyrks

Your gateway to the world of music lyrics.

Product

Features


© 2026 Lyrks. All rights reserved.